Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zitatha izi ndinapenya, taonani, khamu lalikuru, loti palibe munthu anakhozakuliwerenga, ocokera mwa mtundu uti wonse, ndi mafuko ndi anthu ndi manenedwe, akuimirira ku mpando wacifumu ndi pamaso pa Mwanawankhosa, atabvala zobvalazoyera, ndi makhwatha a kanjedza m'manja mwao;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 7

Onani Cibvumbulutso 7:9 nkhani