Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 7:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo angelo onse anaimirira pozinga mpando wacifumu, ndi akulu, ndi zamoyozo zinai; ndipo anagwa nkhope yao pansi ku mpando wacifumu, nalambifa Mulungu,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 7

Onani Cibvumbulutso 7:11 nkhani