Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zitatha izi ndinao na angelo anai alinkuimirira pa ngondya zinai za dziko, akugwira mphepo zinai za dziko, kuti ingaombe mphepo padziko, kapena panyanja, kapena pa mtengo uli wonse.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 7

Onani Cibvumbulutso 7:1 nkhani