Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 6:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinapenya, taonani, kavalo wotumbuluka; ndipo iye womkwera, dzina lace ndiye Imfa; ndipo Hade anatsatana naye; ndipo anawapatsa ulamuliro pa dera lacinai la dziko, kukapha ndi lupanga, ndi njala, ndi imfa, ndi zirombo za padziko.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 6

Onani Cibvumbulutso 6:8 nkhani