Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona m'dzanja lamanja la iye wakukhala pa mpando wacifumu buku lolembedwa m'kati ndi kunja kwace, losindikizika ndi zizindikilo zisanu ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 5

Onani Cibvumbulutso 5:1 nkhani