Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Zitatha izi ndinapenya, ndipo taonani, khomo lotseguka m'Mwamba, ndipo mau oyamba ndinawamva, ngati lipenga Iakulankhuia ndi ine, anati, Kwera kuno, ndipo ndidzakuonetsa zimene ziyenera kucitika m'tsogolomo.

2. Pomwepo ndinakhala mwa Mzimu; ndipo, taonani padaikika mpando wacifumu m'Mwamba ndi pa mpandowo padakhala wina;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 4