Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa unena kuti ine ndine wolemera, ndipo cuma ndiri naco, osasowa kanthu; ndipo sudziwa kuti ndiwe watsoka, ndi wocititsa cifundo, ndi wosauka, ndi wakhungu, ndi wausiwa;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 3

Onani Cibvumbulutso 3:17 nkhani