Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 22:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena kwa ine, Tapenya, usacite; ndine kapolo mnzako, ndi mnzao wa abale ako aneneri, ndi wa iwo akusunga mau a buku ili; lambira Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 22

Onani Cibvumbulutso 22:9 nkhani