Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 22:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena, Idzani, Ndipo wakumva anene, Idzani. Ndipo wakumva ludzu adze; iye wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 22

Onani Cibvumbulutso 22:17 nkhani