Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 21:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa ine, Zatha. Ine ndine Alefa ndi Omega, woyamba ndi wotsiriza. Kwa iye wakumva ludzu ndidzampatsa amwe ku kasupe wa madzi a moyo kwaulere.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:6 nkhani