Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 21:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

acisanu, ndi sardoau; acisanu ndi cimodzi, ndi sardiyo; acisanu ndi ciwiri, ndi krusolito; acisanu ndi citatu, ndi berulo; acisanu ndi cinai, ndi topaziyo; akhumi, ndi krusoprazo; akhumi ndt cimodzi, ndi huakinto; akhumi ndi ciwiri, ndi ametusto.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:20 nkhani