Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 20:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona mipando yacifumu, ndipo anakhala pamenepo; ndipo anawapatsa ciweruziro; ndipo ndinaona mizimu ya iwo amene adawadula khosi cifukwa ca umboni wa Yesu, ndi cifukwa ca mau a Mulungu, ndi iwo amene sanalambira cirombo, kapena fano lace, nisanalandira lembalo pamphumi ndi pa dzanja lao; ndipo anakhala ndi moyo, nacita ufumu pamodzi ndi Kristu zaka cikwi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 20

Onani Cibvumbulutso 20:4 nkhani