Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 20:13-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Ndipo nyanja inapereka akufawo anali momwemo, ndipo imfa ndi Hade zinapereka akufawo anali m'menemo; ndipo anaweruzidwa yense monga mwa nchito zace,

14. Ndipo imfa ndi Hade zinaponyedwa m'nyanja yamoto. Iyo ndiyo imfa yaciwiri, ndiyo nyanja yamoto.

15. Ndipo ngati munthu sanapezedwa wolembedwa m'buku la moyo, anaponyedwa m'nyanja yamoto.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 20