Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 20:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo ndinaona mngelo anatsika Kumwamba, nakhala naco cifungulo ca phompho, ndi unyolo waukuru m'dzanja lace.

2. Ndipo anagwira cinjoka, njoka yakaleyo, ndiye mdierekezi ndi Satana, nammanga iye zaka cikwi,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 20