Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidziwa cisautso cako, ndi umphawi wako (komatu uli wacuma), ndi mwano wa iwo akunena za iwo okha kuti ali Ayuda, osakhala Ayuda, komatu sunagoge wa Satana.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 2

Onani Cibvumbulutso 2:9 nkhani