Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 18:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ndi vinyo wa mkwiyo wa cigololo cace mitundu yonse idagwa; ndipo mafumu a dziko anacita naye cigololo; ndipo ocita malonda a dziko analemera ndi mphamvu ya kudyererakwace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:3 nkhani