Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 18:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1 ndi kuunika kwa nyali sikudzaunikiranso konse mwa iwe; ndi mau a mkwati ndi a mkwatibwi sadzamvekanso konse mwa iwe; pakuti otsatsa malonda anu anali omveka a m'dziko; pakuti 2 ndi nyanga yako mitunduyonse inasokeretsedwa.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:23 nkhani