Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 18:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anathira pfumbi pamitu pao, napfuula, ndi kulira, ndi kucita maliro, nanena, Tsoka, tsoka, mudzi waukuruwo, umene analemerezedwa nao onse akukhala nazo zombo panyanja, cifukwa ca kulemera kwace, pakuti m'ora limodzi unasanduka bwinja.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:19 nkhani