Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 17:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo adzacita nkhondo pa Mwanawankhosa, ndipo Mwanawankhosa adzawalaka, cifukwa ali Mbuye wa ambuye, ndi Mfumu ya mafumu; ndipo adzawalakanso iwo akukhala naye, oitanidwa, ndi osankhika ndi okhulupirika.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 17

Onani Cibvumbulutso 17:14 nkhani