Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 16:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenthedwa anthu ndi kutentha kwakukuru; ndipo anacitira mwano dzina la Mulungu wokhala nao ulamuliro pa miliri iyi; ndipo sanalapa kuti amcitire ulemu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16

Onani Cibvumbulutso 16:9 nkhani