Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 16:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo 5 anatsika kumwamba matalala akuru, lonse lolemera ngati talenti, nagwa pa anthu; ndipo anthu 6 anacitira Mulungu mwano cifukwa ca mliri wa matalala, pakuti m1iri wace nm waukuru ndithu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16

Onani Cibvumbulutso 16:21 nkhani