Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 16:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo 2 cimudzi cacikuruco cidagawika patatu, ndi midzi ya amitundu inagwa; ndipo 3 Babulo waukuru unakumbukika pamaso pa Mulungu, kuti aupatse cikho ca vinyo wamkali wa mkwiyo wace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16

Onani Cibvumbulutso 16:19 nkhani