Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 14:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ayimba ngati nyimbo yatsopane ku mpando wacifumu, ndi pamaso pa zamoyo zinai, ndi akulu; ndipo palibe munthu anakhoza kuphunzira nyimboyi, kama zikwi zana mphambu makumi anai kudza anai, ogulidwa kucokera kudziko.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 14

Onani Cibvumbulutso 14:3 nkhani