Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 14:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinapenya, taonani, Mwanawankhosayo alikuimirira pa phiri la Ziyoni, ndipo pamodzi ndi iye zikwi zana mphambu makumi anai kudza anai, akukhala nalo dzina lace ndi dzina la Atate wace lolembedwa pamphumi pao.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 14

Onani Cibvumbulutso 14:1 nkhani