Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 13:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pano pali nzeru. Iye wakukhala naco cidziwitso awerenge ciwerengero ca ciromboco; pakuti ciwerengero cace ndi ca munthu; ndipo ciwerengero cace ndico mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu ndi cimodzi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 13

Onani Cibvumbulutso 13:18 nkhani