Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cisokeretsa iwo akukhala padziko ndi zizindikilo zimene anacipatsa mphamvu yakuzicita pamaso pa cirombo, ndi kunena kwa iwo akukhala padziko, kuti apange fane la ciromboco, cimene cinali nalo bala la lupanga nicinakhalanso ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 13

Onani Cibvumbulutso 13:14 nkhani