Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 12:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo cizindikilo cacikuru cinaoneka m'mwamba; mkazi wobvekedwa dzuwa, ndi mwezi ku mapazi ace, ndi pamutu pace korona wa nyenyezi khumi ndi ziwiri;

2. ndipo anali ndi pakati; ndipo apfuula alimkubala, ndi kumva zowawa zakubala.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12