Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 10:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nalumbira kuchula iye amene ali ndi moyo ku nthawi za nthawi, amene analenga m'mwamba ndi zinthu ziri momwemo, ndi dziko lapansi ndi zinthu ziri momwemo, ndi nyanja ndi zinthu ziri momwemo kuti sipadzakhalanso nthawi:

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 10

Onani Cibvumbulutso 10:6 nkhani