Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 1:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

CIBVUMBULUTSO ca Yesu Kristu, cimene Mulungu anambvumbulutsira acionetsere akapolo ace, ndico ca izi ziyenera kucitika posacedwa: ndipo potuma mwa mngelo wace anazindikiritsa izi kwa kapolo wace Yohane;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 1

Onani Cibvumbulutso 1:1 nkhani