Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 8:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo si cotero cokha, koma ife tomwe, tiri nazo zoundukula za Mzimu, inde ifenso tibuula m'kati mwathu, ndi kulindirira umwana wathu, ndiwo ciomboledwe ca thupi lathu.

Werengani mutu wathunthu Aroma 8

Onani Aroma 8:23 nkhani