Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 8:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ngati ana, pomweponso olowa nyumba; inde olowa nyumba ace a Mulungu, ndi olowa anzace a Kristu; ngatitu ife timva zowawa pamodzi naye, kuti tikalaodirenso ulemerero pamodzi ndi iye.

Werengani mutu wathunthu Aroma 8

Onani Aroma 8:17 nkhani