Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 7:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiyamika Mulungu, mwa Yesu Kristu Ambuye wathu. Ndipo cotero ine ndekha ndi mtimatu nditumikira cilamulo ca Mulungu; koma ndi thupi nditumikira lamulo la ucimo.

Werengani mutu wathunthu Aroma 7

Onani Aroma 7:25 nkhani