Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 6:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndilankhula manenedwe a anthu, cifukwa ca kufoka kwa thupi lanu; pakuti monga inu munapereka ziwalo zanu zikhale akapolo a conyansa ndi a kusayeruzika kuti zicite kusayeruzika, inde kotero tsopano perekani ziwalo zanu zikhale akapolo a cilungamo kuti zicite ciyeretso.

Werengani mutu wathunthu Aroma 6

Onani Aroma 6:19 nkhani