Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo musapereke ziwalo zanu kuucimo, zikhale zida za cosalungama; koma mudzipereke inu nokha kwa Mulungu, monga amoyo ataturuka mwa akufa, ndi ziwalo zanu kwa Mulungu zikhale zida za cilungamo,

Werengani mutu wathunthu Aroma 6

Onani Aroma 6:13 nkhani