Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 5:20-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Ndipo lamulo linalowa moyenjezera, kuti kulakwa kukacuruke; koma rl pamene ucimo unacuruka, pomwepo cisomo cinacuruka koposa;

21. kuti, mongaucimo unacita ufumu muimfa, comweconso cisomo cikacite ufumu mwa cilungamo, kufikira moyo wosatha mwa Yesu Kristu Ambuye wathu.

Werengani mutu wathunthu Aroma 5