Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 5:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ngati, ndi kulakwa kwa mmodzi, imfa inacita ufumu mwa mmodziyo; makamaka ndithu amene akulandira kucuruka kwace kwa cisomo ndi kwa mphatso ya cilungamo, adzacita ufumu m'moyo mwa mmodzi, ndiye Yesu Kristu.

Werengani mutu wathunthu Aroma 5

Onani Aroma 5:17 nkhani