Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 3:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo potero Myuda aposa Dinji? Kapena mdulidwe upindulanji?

2. Zambiri monse monse: coyamba, kuti mau a Mulungu anaperekedwa kwa iwo.

3. Nanga bwanji ngati ena sanakhulupira? Kodi kusakhulupira kwao kuyesa cabe cikhulupiriko ca Mulungu?

Werengani mutu wathunthu Aroma 3