Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 2:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cifukwa cace uli wopanda mau owiringula, munthu iwe, amene uli yense wakuweruza; pakuti m'mene uweruza wina, momwemo udzitsutsa iwe wekha, pakuti iwe wakuweruza, umacita zomwezo.

2. Ndipo tidziwa kuti kuweruza kwa Mulungu kuli koona pa iwo akucita zotere.

Werengani mutu wathunthu Aroma 2