Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 14:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo iye amene ali wofoka m'cikhulupiriro, mumlandire, koma si kucita naye makani otsutsana ai.

2. Munthu mmodzi akhulupirira kuti adye zinthu zonse, koma wina wofoka angodya zitsamba.

3. Wakudyayo asapeputse wosadyayo; ndipo wosadyayo asaweruze wakudyayo; pakuti Mulungu wamlandira.

Werengani mutu wathunthu Aroma 14