Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 13:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo citani ici, podziwa inu nyengo, kuti tsopano ndiyo nthawi yabwino yakuuka kutulo; pakuti tsopano cipulumutso cathu ciri pafupi koposa pamene tinayamba kukhulupira.

Werengani mutu wathunthu Aroma 13

Onani Aroma 13:11 nkhani