Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 11:30-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Pakuti 2 monga inunso kale simunamvera Mulungu, koma tsopano mwalandira cifundo mwa kusamvera kwao,

31. coteronso iwo sanamvera tsopano, kuti iwonso akalandire cifundo, cifukwa ca cifundo ca kwa inu.

32. Pakuti 3 Mulungu anatsekera pamodzi onse m'kusamvera, kuti akacitire onse cifundo.

Werengani mutu wathunthu Aroma 11