Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 11:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ngati iwe unasadzidwa ku mtengo wazitona wa mtundu wa kuthengo, ndipo unamezetsanidwa ndi mtengo wazitona wabwino, mokaniza makhalidwe ako; koposa kotani nanga iwo, ndiwo nthambi za mtundu wace, adzamezetsanidwa ndi mtengo wao womwewo wazitona?

Werengani mutu wathunthu Aroma 11

Onani Aroma 11:24 nkhani