Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kwa onse a ku Roma, okondedwa a Mulungu, oitanidwa kuti akhale oyera mtima: Cisomo cikhale ndinu ndi mtendere wa kwa Mulungu Atate wathu, ndi Ambuye Yesu Kristu.

Werengani mutu wathunthu Aroma 1

Onani Aroma 1:7 nkhani