Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti cilengedwere dziko lapansi zaoneka bwino zosaoneka zace ndizo mphamvu yace yosatha ndi umulungu wace; popeza zazindikirika ndi zinthu zolengedwa, kuti iwo adzakhale opanda mau akuwiringula;

Werengani mutu wathunthu Aroma 1

Onani Aroma 1:20 nkhani