Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 1:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. PAULO, kapolowa Yesu Kristu, mtumwi woitanidwa, wopatulidwa kukanena Uthenga Wabwino wa Mulungu,

2. umene iye analonjeza kale ndi mau a ananeri ace m'malembo oyera,

3. wakunena za Mwana wace, amene anabadwa, wa mbeu ya Davide, monga mwa thupi,

Werengani mutu wathunthu Aroma 1