Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Akolose 3:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace bvalani, monga osankhika a Mulungu, oyera mtima ndi okondedwa, mtima wacifundo, kukoma mtima, kudzicepetsa, cifatso, kuleza mtima;

Werengani mutu wathunthu Akolose 3

Onani Akolose 3:12 nkhani