Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Akolose 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa ici ifenso, kuyambira tsiku limene tidamva, sitileka kupembedzera ndi kupempherera inu, kuti mukadzazidwe ndi cizindikiritso ca cifuniro cace mu nzeru zonse ndi cidziwitso ca mzimu,

Werengani mutu wathunthu Akolose 1

Onani Akolose 1:9 nkhani