Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Akolose 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti mwa iye, zinalengedwa zonse za m'mwamba, ndi za padziko, zooneka ndi zosaonekazo, kapena mipando yacifumu, kapena maufumu, kapena maukulu, kapena maulamuliro; zinthu zonse zinalengedwa mwa iye ndi kwa iye.

Werengani mutu wathunthu Akolose 1

Onani Akolose 1:16 nkhani