Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 9:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma kulowa m'caciwiri, mkuru wa ansembe yekha kamodzi pacaka, wosati wopanda mwazi, umene apereka cifukwa ca iye yekha, ndi zolakwa za anthu;

Werengani mutu wathunthu Ahebri 9

Onani Ahebri 9:7 nkhani