Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 9:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kotero 10 Kristunso ataperekedwa nsembe kamodzi kukasenza macimo a ambiri, 11 adzaonekera pa nthawi yaciwiri, wopanda ucimo, kwa iwo amene amlindirira, kufikira cipulumutso.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 9

Onani Ahebri 9:28 nkhani